Malawi Voice Accounts The Good Side Of MCP:We Tell You The Evil Side Of The Crocodiles Party

Bravo Malawi Voice on MCP post, but you have just talked of good things MCP contributed to Malawi, koma what about;

 1. Nkhaza za a MYP komanso a Yufi?
 2. Nyakula?
 3. Dziwe lang’ona?
 4. Imfa ya Matenje, Imfa ya Gadama and friends?
 5. Makako ku Zomba?
 6. Ndende ya udzudzu ya Nsanje?
 7. Mikuyu Prison?
 8. A Yufi kugwilira adzikazi athu?
 9. Cabinet Crisis?
 10. Deportation of Jehovah’s Witness Followers?
 11. Compulsory MCP membership cards,
 12. Achamwaka,
 13. Death of democracy in 1965 after MCP gained power?
 14. Waiwala kutinso ana amalephera kulemba Mayeso chifukwa chopanda khadi
 15. Mzimai akakhala ndi mimba mwana osabadwayo amamudulira khadi
 16. Azibambo ngati sanakhome nsonkho kunali kumangidwa nyakula.
 17. A youth amagwilira azimai nkona lero tiri ndi anthu a AIDS chifukwa cha MCP.
 18. Kamuzu akamabwera dera lanu timalandidwa mbuzi, nkhumba, abakha, amphaka.
 19. Timatulusidwa mkalasi kumakaimba mmanja kunseu mpaka kamuzu adutse.
 20. Pioneer inali yamphamvu kuposa Army.
 21. Ukadana ndi kamuzu amakakudyetsa Ku ng’ona Ku Stella Maris
 22. Ukadana ndi Kamuzu umakhomedwa misomali mmutu, ngakhale mutawafunsa a T/A Chikumbu.
 23. Ma points pa form 4 Kamuzu amaletsa distinction in agriculture.
 24. Tv sitimaloledwa kuonera.
 25. Kunalibe ma minibus
 26. Ma cellular phone kunalibe
 27. Linali boma loipa, bola lero tikumutukwana President Mutharika no mlandu koma kale monga achitira Chakwera kutukwana President bwenzi atadyedwa kale ndi ng’ona
 28. Wapantchito akamamanga nyumbayabwino amapasidwa kaye ntchito kut afufuzidwe
 29. Okana kudula khadi monga Amboni za Yehova amaphedwa nkukapasira ng’ona kuti zikadye kotero kut ng’ona zanthawi imeneyo zinali zosangalala komanso zathanzi sizapanozi ai
 30. Ma wayilesi ena amaletsa, wayilesi idali MBC Radio 1 basi
 31. Kampani ya nyuzipepa idali imodzi yokha basi yomwe imatulutsa Malawi News
 32. All these are products of MCP, when they come to power they will bring them back because it’s their developments.

4 comments

 • You fools its not about MCP but Kamuzu
  Anyway just imagine kut Kamuzu was from DPP would u blame DPP or Kamuzu?????????

  • William wake up! Malawi must never be ruled by MCP again, no matter how much they “rebrand”. It has blood on its hands. The world will look upon us with shock and wonder if Malawians are crazy. The Nazi Party can never rule Germany again. National Party will never rule South Africa again. So why should MCP rule Malawi again? Are we that poor that we can allow an oppressor to come back under the guise of rebranding? No!

 • Please remind the people and educate the young ones. Chakwera thinks he can erase history, he thinks Malawians are fools. Dredge up all the history, they are calling it propaganda but its actually facts. Remind the people. Start with Chilobwe Murders and go on from there.

Leave a Reply

Fill in your details below or click an icon to log in:

WordPress.com Logo

You are commenting using your WordPress.com account. Log Out / Change )

Twitter picture

You are commenting using your Twitter account. Log Out / Change )

Facebook photo

You are commenting using your Facebook account. Log Out / Change )

Google+ photo

You are commenting using your Google+ account. Log Out / Change )

Connecting to %s